1 Ndalowa m'munda mwanga, mlongwanga, mkwatibwi:Ndachera nipa yanga ndi zonunkhiritsa zanga;Ndadya uci wanga ndi cisa cace;Ndamwa vinyo wanga ndi mkaka wanga.Idyani, atsamwalinu,Imwani, mwetsani cikondi.
Werengani mutu wathunthu Nyimbo 5
Onani Nyimbo 5:1 nkhani