Nyimbo 5:2 BL92

2 Ndinagona tulo, koma mtima wanga unali maso:Ndi mau a bwenzi langa mnyamatayo agogoda, nati,Nditsegulire, mlongwanga, wokondedwa wanga, nkhunda yanga, wangwiro wanga:Pakuti pamtu panga padzala mame,Patsitsi panga pali madontho a usiku.

Werengani mutu wathunthu Nyimbo 5

Onani Nyimbo 5:2 nkhani