6 Ndinamtsegulira bwenzi langalo;Koma ndinampeza, bwenzi langa atacoka.Moyo wanga unalefuka polankhula iye:Ndinamfunafuna, osampeza;Ndinamuitana, koma sanandibvomera.
Werengani mutu wathunthu Nyimbo 5
Onani Nyimbo 5:6 nkhani