17 Ndipo kwa Mfumu yosatha, yosabvunda, yosaoneka, Mulungu wa yekha, ukhale ulemu ndi ulemerero, kufikira nthawi za nthawi. Amen.
Werengani mutu wathunthu 1 Timoteo 1
Onani 1 Timoteo 1:17 nkhani