Ahebri 10:8 BL92

8 Pakunena pamwamba apa, kuti, Nsembe ndi zopereka ndi nsembe zopsereza zamphumphu ndi za kwa macimo simunazifuna, kapena kukondwera nazo (zimene ziperekedwa monga mwa lamulo),

Werengani mutu wathunthu Ahebri 10

Onani Ahebri 10:8 nkhani