6 koma wopanda cikhulupiriro sikutheka kumkondweretsa; pakuti iye wakudza kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti alipo, ndi kuti ali wobwezera mphotho iwo akumfuna iye.
Werengani mutu wathunthu Ahebri 11
Onani Ahebri 11:6 nkhani