9 Komanso, tinali nao atate a thupi lathu akutilanga, ndipo tinawalemekeza; kodi sitidzagonjera Atate wa mizimu koposa nanga, ndi kukhala ndi moyo?
Werengani mutu wathunthu Ahebri 12
Onani Ahebri 12:9 nkhani