11 Pakuti matupi a nyama zija, mwazi wa izo umatengedwa ndi mkulu wa ansembe kulowa m'malo opatulidwa, cifukwa ca zoipa, amatenthedwa kunja kwa tsasa.
Werengani mutu wathunthu Ahebri 13
Onani Ahebri 13:11 nkhani