5 Mtima wanu ukhale wosakonda cuma; zimene muli nazo zikukwanireni; pakuti iye anati, Sindidzakusiya konse, kungakhale kukutaya, sindidzakutaya ndithu.
Werengani mutu wathunthu Ahebri 13
Onani Ahebri 13:5 nkhani