7 Kumbukilani atsogoleri anu, amene analankhula nanu Mau a Mulungu; ndipo poyang'anira citsiriziro ca mayendedwe ao mutsanze cikhulupiriro cao.
Werengani mutu wathunthu Ahebri 13
Onani Ahebri 13:7 nkhani