9 Musatengedwe ndi maphunzitso a mitundu mitundu, ndi acilendo; pakuti nkokoma kuti mtima ukhazikike ndi cisomo; kosati ndi zakudya, zimene iwo adazitsata sanapindula nazo.
Werengani mutu wathunthu Ahebri 13
Onani Ahebri 13:9 nkhani