15 Pakuti sitiri naye mkulu wa ansembe wosatha kumva cifundo ndi zofoka zathu; koma wayesedwa m'zonse monga momwe ife, koma wopanda ucimo.
Werengani mutu wathunthu Ahebri 4
Onani Ahebri 4:15 nkhani