Ahebri 4:2 BL92

2 Pakuti kwa ifenso walalikidwa Uthenga Wabwino, monganso kwa iwo; koma iwowa sanapindula nao mau omvekawo, popeza sanasanganizika ndi cikhulupiriro mwa iwo amene adawamva.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 4

Onani Ahebri 4:2 nkhani