25 kucokera komwekoakhoza kupulumutsa konse konse iwo akuyandikira kwa Mulungu mwa iye, popeza ali nao moyo wace cikhalire wa kuwapembedzera iwo.
Werengani mutu wathunthu Ahebri 7
Onani Ahebri 7:25 nkhani