Ahebri 7:3 BL92

3 wopanda atate wace, wopanda amace, wopanda mawerengedwe a cibadwidwe cace, alibe ciyambi ca masiku ace kapena citsiriziro ca moyo wace, wofanizidwa ndi Mwana wa Mulungu), iyeyu wakhala wansembe kosalekeza.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 7

Onani Ahebri 7:3 nkhani