6 koma iye amene mawerengedwe a cibadwidwe cace sacokera mwa iwo, anatenga limodzi la magawo khumi kwa Abrahamu, namdalitsa iye amene ali nao malonjezano.
Werengani mutu wathunthu Ahebri 7
Onani Ahebri 7:6 nkhani