Ahebri 8:11 BL92

11 Ndipo sadzaphunzitsa yense mfulu mnzace,Ndipo yense mbale wace, ndi kuti, Zindikira Ambuye:Pakuti onse adzadziwa Ine, Kuyambira wamng'ono kufikira wamkuru wa iwo.

Werengani mutu wathunthu Ahebri 8

Onani Ahebri 8:11 nkhani