Ahebri 8:3 BL92

3 Pakuti mkulu wa ansembe ali yense aikidwa kupereka mitulo, ndiponso nsembe; potero nkufunika kuti ameneyo akhale nako kanthunso kakupereka,

Werengani mutu wathunthu Ahebri 8

Onani Ahebri 8:3 nkhani