14 koma ndidzayatsa moto pa linga la Raba, udzanyeketsa nyumba zacifumu zace, ndi kupfuula tsiku la nkhondo, ndi namondwe, tsiku la kabvumvulu;
Werengani mutu wathunthu Amosi 1
Onani Amosi 1:14 nkhani