2 Ndipo anati, Yehova adzadzuma ali m'Ziyoni, nadzamveketsa mau ace ali m'Yerusalemu; podyetsa abusa padzacita cisoni, ndi mutu wa Karimeli udzauma.
Werengani mutu wathunthu Amosi 1
Onani Amosi 1:2 nkhani