6 Atero Yehova, Cifukwa ca zolakwa zitatu za Gaza, kapena zinai, sindidzabweza kulanga kwace; popeza anatenga ndende anthu onse kuwapereka kwa Edomu;
Werengani mutu wathunthu Amosi 1
Onani Amosi 1:6 nkhani