1 Atero Yehova, Cifukwa ca zolakwa zitatu za Moabu, kapena zinai, sindidzabweza kulanga kwace; popeza anatentha mafupa a mfumu ya ku Edomu asanduke njereza;
Werengani mutu wathunthu Amosi 2
Onani Amosi 2:1 nkhani