Amosi 2:10 BL92

10 Ndipo ndinakukwezani kucokera m'dziko la Aigupto, ndi kukutsogolerani zaka makumi anai m'cipululu, kuti mulandire dziko la Aamori likhale colowa canu.

Werengani mutu wathunthu Amosi 2

Onani Amosi 2:10 nkhani