1 Tamverani mau awa akunenerani Yehova motsutsa, inu ana a Israyeli, kulinenera banja lonse ndinalikweza kuliturutsa m'dziko la Aigupto, ndi kuti,
Werengani mutu wathunthu Amosi 3
Onani Amosi 3:1 nkhani