10 Pakuti sadziwa kucita zolungama, amene akundika zaciwawa ndi umbala m'nyumba zao zacifumu, ati Yehova.
Werengani mutu wathunthu Amosi 3
Onani Amosi 3:10 nkhani