13 Tamverani inu, mucitire umboni wotsutsa nyumba ya Yakobo, ati Ambuye Yehova Mulungu wa makamu.
Werengani mutu wathunthu Amosi 3
Onani Amosi 3:13 nkhani