Amosi 4:6 BL92

6 Ndipo ine ndakupatsaninso mano oyera m'midzi yanu yonse, ndi kusowa mkate m'malo mwanu monse; koma simunabwerera kudza kwa Ine, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Amosi 4

Onani Amosi 4:6 nkhani