12 Pakuti ndidziwa kuti zolakwa zanu nzocuruka, ndi macimo anu ndi olimba, inu akusautsa olungama, akulandira cokometsera mlandu, akukankha osowa kucipata.
Werengani mutu wathunthu Amosi 5
Onani Amosi 5:12 nkhani