19 Kudzakhala monga munthu akathawa mkango, ndi cimbalangondo cikomana naye; kapena akalowa m'nyumba, natsamira kukhoma ndi dzanja lace, nimluma njoka.
Werengani mutu wathunthu Amosi 5
Onani Amosi 5:19 nkhani