Amosi 5:24 BL92

24 Koma ciweruzo ciyende ngati madzi, ndi cilungamo ngati mtsinje wosefuka.

Werengani mutu wathunthu Amosi 5

Onani Amosi 5:24 nkhani