11 Cifukwa cace tsono, ululani kwa Yehova Mulungu wa makolo anu, nimucite comkondweretsa; mudzilekanitse ndi mitundu ya anthu a m'dzikomo, ndi kwa akazi acilendo.
Werengani mutu wathunthu Ezara 10
Onani Ezara 10:11 nkhani