Ezara 10:12 BL92

12 Ndipo unayankha msonkhano wonse, ndi kunena ndi mau akuru, Monga mwa mau anu tiyenera kucita.

Werengani mutu wathunthu Ezara 10

Onani Ezara 10:12 nkhani