Ezara 7:27 BL92

27 Wodala Yehova Mulungu wa makolo athu, amene anaika cinthu cotere mu mtima wa mfumu, kukometsera nyumba ya Yehova iri ku Yerusalemu,

Werengani mutu wathunthu Ezara 7

Onani Ezara 7:27 nkhani