Hoseya 14:3 BL92

3 Asuri sadzatipulumutsa; sitidzayenda pa akavalo, ndipo sitil dzanenanso kwa nchito ya manja athu, Inu ndinu milungu yathu; pakuti mwa Inu ana amasiye apeza cifundo.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 14

Onani Hoseya 14:3 nkhani