Hoseya 14:9 BL92

9 Wanzeru ndani, kuti azindikire izi? waluntha, kuti adziwe izi? pakuti njira za Yehova ziri zoongoka; ndipo olungama adzayendamo, koma olakwa adzagwamo.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 14

Onani Hoseya 14:9 nkhani