Hoseya 2:13 BL92

13 Ndipo ndidzamlanga cifukwa ca masiku a Abaala amene anawafukizira, nabvala mphete za m'mphuno, ndi zokometsera zace, natsata omkonda, nandiiwala Ine, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 2

Onani Hoseya 2:13 nkhani