Hoseya 2:14 BL92

14 Cifukwa cace taonani, ndidzamkopa ndi kumka naye kucipululu, ndi kulankhula naye momkonda mtima.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 2

Onani Hoseya 2:14 nkhani