Hoseya 3:5 BL92

5 atatero ana a Israyeli adzabwera, nadzafuna Yehova Mulungu wao, ndi Davide mfumu yao, nadzafika ndi mantha kwa Yehova, ndi ku ukoma wace masiku otsiriza.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 3

Onani Hoseya 3:5 nkhani