Hoseya 4:2 BL92

2 Koma kulumbira, ndi kunama, ndi kupha, ndi kuba, ndi kucita cigololo; aboola, ndi mwazi ukhudzana nao mwazi.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 4

Onani Hoseya 4:2 nkhani