Hoseya 5:14 BL92

14 Pakuti ndidzakhala kwa Efraimu ngati mkango, ndi kwa nyumba ya Yuda ngati msona wa mkango; ndidzamwetula Ine ndi kucoka; ndidzanyamula, ndipo palibe wakulanditsa.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 5

Onani Hoseya 5:14 nkhani