15 Ndidzamuka ndi kubwerera kumka kumalo kwanga, mpaka adzabvomereza kuparamula kwao, nafunafuna nkhope yanga; m'msauko mwao adzandifunafuna mwacangu.
Werengani mutu wathunthu Hoseya 5
Onani Hoseya 5:15 nkhani