Hoseya 8:1 BL92

1 Lipenga kukamwa kwako, Akudza ngati ciombankhanga, kulim bana ndi nyumba ya Yehova; cifukwa analakwira cipangano canga, napikisana naco cilamulo canga.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 8

Onani Hoseya 8:1 nkhani