Hoseya 8:14 BL92

14 Pakuti Israyeli waiwala Mlengi wace, namanga akacisit ndipo Yuda wacurukitsa midzi yamalinga; koma ndidzatumizira midzi yace moto, nudzatha nyumba zace zazikuru.

Werengani mutu wathunthu Hoseya 8

Onani Hoseya 8:14 nkhani