20 Usatemberere mfumu ngakhale poganizira; usatemberere wolemera m'cipinda cogona iwemo; pakuti mbalame ya mlengalenga idzanyamula mauwo, ndipo couluka ndi mapiko cidzamveketsa zonenazo.
Werengani mutu wathunthu Mlaliki 10
Onani Mlaliki 10:20 nkhani