8 Inde, munthu akakhala ndi moyo zaka zambiri, akondwere ndi zonsezo; koma akumbukire masiku amdima kuti adzacuruka. Zonse zirinkudza ziri zacabe.
Werengani mutu wathunthu Mlaliki 11
Onani Mlaliki 11:8 nkhani