13 Mau atha; zonse zamveka zatha; opa Mulungu, musunge malamulo ace; pakuti coyenera anthu onse ndi ici.
Werengani mutu wathunthu Mlaliki 12
Onani Mlaliki 12:13 nkhani