Mlaliki 12:3 BL92

3 tsikulo omwe asunga nyumba adzanthunthumira, amuna olimba nadzawerama, akupera nadzaleka poperewera, omwe ayang'ana pamazenera nadzadetsedwa;

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 12

Onani Mlaliki 12:3 nkhani