Mlaliki 2:1 BL92

1 Ndinati mumtima mwanga, Tiyetu, ndikuyese ndi cimwemwe; tapenya tsono zabwino; ndipo taona, icinso ndi cabe.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 2

Onani Mlaliki 2:1 nkhani