Mlaliki 2:16 BL92

16 Pakuti wanzerusaposa citsiru kukumbukidwa nthawi zonse; pakuti zonse zooneka kale zidzaiwalika m'tsogolomo, Ndipo wanzeru amwalira bwanji ngati citsirutu.

Werengani mutu wathunthu Mlaliki 2

Onani Mlaliki 2:16 nkhani