19 Ndipo ndani adziwa ngati adzakhala wanzeru pena citsiru? Koma adzalamulira nchito zanga zonse ndinasauka nazo, ndi kuzigwira mwanzeru kunja kuno. Icinso ndi cabe.
Werengani mutu wathunthu Mlaliki 2
Onani Mlaliki 2:19 nkhani